MERA YATSUTSA ZA KWERA KWA MAFUTA A GALIMOTO

 By Stanley Chiputu

Bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority ( MERA) lasutsa mphekesera zomwe zikumveka kuti liri ndi malingaliro  okweza mitengo ya mafuta a galimoto.

Mu Chikalata chomwe bungweli latulutsa ilo lati malipoti abodzawa akufuna kubweretsa chisokonezo popeza anthu agula mafuta mwaphuma.

Mulipotili nso ilo lati dziko muno muli mafuta okwanila.




Comments

  1. Mafuta ndi okwaniradi mdziko muno, ndi chifukwa chake magalimoto akumafola zimizere mu ma filling station

    ReplyDelete
  2. Nde mwati mafuta ndokwanira🤔🤔🤔

    ReplyDelete

Post a Comment

Popular posts from this blog

MULTI-CHOICE TO RESUME DSTV SERVICES IN MALAWI

MACRA TO HOST SPACE CONFERENCE IN OCTOBER

ARSENAL STAR, ZINCHENKO CLAIMS PARTEY AS A BEST MIDFIELDER